2 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone, ndipo imvani mawu a Senakeribu amene watumiza kudzatonza nawo+ Mulungu wamoyo. Salimo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani! Diso la Yehova lili pa anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha,+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+
16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone, ndipo imvani mawu a Senakeribu amene watumiza kudzatonza nawo+ Mulungu wamoyo.
18 Taonani! Diso la Yehova lili pa anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha,+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+