1 Mafumu 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mumve pemphero lopempha chifundo la mtumiki wanu komanso la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayangʼana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ mumve nʼkukhululuka.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:30 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,4/2011, tsa. 28
30 Mumve pemphero lopempha chifundo la mtumiki wanu komanso la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayangʼana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ mumve nʼkukhululuka.+