6 Pakuti tsiku lidzafika, pamene alonda amene ali m’mapiri a Efuraimu adzafuula kuti, ‘Nyamukani amuna inu, tiyeni tipite ku Ziyoni, kwa Yehova Mulungu wathu.’”+
23 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’masiku amenewo, amuna 10 ochokera m’zilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira+ chovala cha munthu amene ndi Myuda+ ndi kunena kuti: “Anthu inu tipita nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+