Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.” Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,7/15/2004, tsa. 18
6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”