Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+

      N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+

  • Yesaya 54:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+

  • Mika 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu ochokera m’mitundu yosiyanasiyana adzabwera n’kunena kuti: “Bwerani+ anthu inu. Tiyeni tipite kukakwera phiri la Yehova. Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo.+ Iye akatiphunzitsa njira zake,+ ndipo ife tidzayenda m’njira zakezo.”+ Pakuti mu Ziyoni mudzatuluka malamulo ndipo mawu a Yehova adzatuluka mu Yerusalemu.+

  • Yohane 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yesu anawayankha kuti: “Zimene ine ndimaphunzitsa si zanga ayi, koma ndi za amene anandituma.+

  • Machitidwe 10:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Chotero ndinawatumiza mwamsanga kwa inu, ndipo mwachita bwino kubwera kuno. N’chifukwa chake pa nthawi ino tonse tili pano pamaso pa Mulungu, kuti timve zonse zimene Yehova wakulamulani kuti mutiuze.”+

  • 1 Atesalonika 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma za kukonda abale,+ n’zosafunika kuti tizichita kukulemberani pakuti inu nomwe, Mulungu amakuphunzitsani+ kukondana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena