2 Mbiri 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumve mapemphero ochonderera a mtumiki+ wanu ndi a anthu anu Aisiraeli, pamene akupemphera atayang’ana malo ano.+ Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ ndipo mumve n’kukhululuka.+ Salimo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana,+Waona ana onse a anthu.+
21 Mumve mapemphero ochonderera a mtumiki+ wanu ndi a anthu anu Aisiraeli, pamene akupemphera atayang’ana malo ano.+ Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ ndipo mumve n’kukhululuka.+