2 Mbiri 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 inuyo mumve muli kumwamba pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo,+ ndipo muwachitire chilungamo.+ Salimo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzafuulira Yehova mokweza,Ndipo iye adzandiyankha m’phiri lake loyera.+ [Seʹlah.] Salimo 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa mwandiweruzira mlandu wanga ndi dandaulo langa.+Mwakhala pampando wachifumu ndipo mukuweruza mwachilungamo.+
35 inuyo mumve muli kumwamba pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo,+ ndipo muwachitire chilungamo.+
4 Chifukwa mwandiweruzira mlandu wanga ndi dandaulo langa.+Mwakhala pampando wachifumu ndipo mukuweruza mwachilungamo.+