Nehemiya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.” Yeremiya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yuda akulira maliro+ ndipo zipata zake zagwetsedwa.+ Zagwetsedwa pansi+ ndipo kulira kwa Yerusalemu kwamveka kumwamba.+
3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.”
2 Yuda akulira maliro+ ndipo zipata zake zagwetsedwa.+ Zagwetsedwa pansi+ ndipo kulira kwa Yerusalemu kwamveka kumwamba.+