Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+

  • Maliro 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+

      Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*

      Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.

  • Hoseya 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+

  • Yoweli 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena