Yeremiya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wanena kuti: “Zidzachitika pa tsikulo kuti mfumu sidzalimba mtima,+ chimodzimodzinso akalonga ake. Ansembe adzagwidwa ndi mantha ndipo aneneri adzadabwa.”+
9 Yehova wanena kuti: “Zidzachitika pa tsikulo kuti mfumu sidzalimba mtima,+ chimodzimodzinso akalonga ake. Ansembe adzagwidwa ndi mantha ndipo aneneri adzadabwa.”+