Yesaya 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu inu, dabwani ndipo chitani kukamwa yasa!+ Matani maso anu kuti musaone.+ Iwo aledzera,+ koma osati ndi vinyo. Akudzandira, koma osati chifukwa cha chakumwa choledzeretsa.+ Machitidwe 13:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 ‘Inu onyoza zimene ine ndikuchita, mudzaona zimene ndikuchitazo ndi kudabwa nazo. Kenako mudzazimiririka, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pang’ono zimene ndidzachite m’masiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+
9 Anthu inu, dabwani ndipo chitani kukamwa yasa!+ Matani maso anu kuti musaone.+ Iwo aledzera,+ koma osati ndi vinyo. Akudzandira, koma osati chifukwa cha chakumwa choledzeretsa.+
41 ‘Inu onyoza zimene ine ndikuchita, mudzaona zimene ndikuchitazo ndi kudabwa nazo. Kenako mudzazimiririka, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pang’ono zimene ndidzachite m’masiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+