2 Mafumu 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gulu lankhondo la Akasidi+ linayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo linaipeza+ m’chipululu cha Yeriko.+ Pamenepo gulu lonse lankhondo la mfumuyo linabalalika n’kuisiya yokha.
5 Gulu lankhondo la Akasidi+ linayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo linaipeza+ m’chipululu cha Yeriko.+ Pamenepo gulu lonse lankhondo la mfumuyo linabalalika n’kuisiya yokha.