Yeremiya 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma tamverani mawu a Yehova akazi inu, ndipo mutchere khutu ku mawu otuluka m’kamwa mwake. Kenako muphunzitse ana anu aakazi kulira maliro+ ndipo mkazi aliyense aphunzitse mnzake nyimbo yoimba polira.+
20 Koma tamverani mawu a Yehova akazi inu, ndipo mutchere khutu ku mawu otuluka m’kamwa mwake. Kenako muphunzitse ana anu aakazi kulira maliro+ ndipo mkazi aliyense aphunzitse mnzake nyimbo yoimba polira.+