2 Samueli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Davide anayamba kuimba nyimbo iyi yoimba polira,+ pamene anali kulira Sauli ndi Yonatani mwana wake.+ Yeremiya 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Meta tsitsi lako lalitalilo ndi kulitaya.+ Ukwere pamapiri opanda mitengo ndi kuimba nyimbo yoimba polira pamenepo,+ pakuti Yehova wakana+ ndi kusiya mbadwo wa anthu amene wawakwiyira.+
17 Ndiyeno Davide anayamba kuimba nyimbo iyi yoimba polira,+ pamene anali kulira Sauli ndi Yonatani mwana wake.+
29 “Meta tsitsi lako lalitalilo ndi kulitaya.+ Ukwere pamapiri opanda mitengo ndi kuimba nyimbo yoimba polira pamenepo,+ pakuti Yehova wakana+ ndi kusiya mbadwo wa anthu amene wawakwiyira.+