Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+ Deuteronomo 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisire nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji.Pakuti iwo ndi m’badwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisire nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji.Pakuti iwo ndi m’badwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+