Deuteronomo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+ Yesaya 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndatambasula manja anga tsiku lonse kwa anthu amakani,*+ amene akuyenda m’njira yoipa+ potsatira maganizo awo,+ Mateyu 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”
5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+
2 “Ndatambasula manja anga tsiku lonse kwa anthu amakani,*+ amene akuyenda m’njira yoipa+ potsatira maganizo awo,+
17 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”