Deuteronomo 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisira nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji. Chifukwa iwo ndi mʼbadwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+
20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisira nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji. Chifukwa iwo ndi mʼbadwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+