Deuteronomo 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisire nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji.Pakuti iwo ndi m’badwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+
20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisire nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji.Pakuti iwo ndi m’badwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+