1 Samueli 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Sauli, ana ake atatu, ndi womunyamulira zida komanso asilikali ake onse, anafera limodzi pa tsiku limenelo.+
6 Chotero Sauli, ana ake atatu, ndi womunyamulira zida komanso asilikali ake onse, anafera limodzi pa tsiku limenelo.+