1 Samueli 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova aperekanso Isiraeli pamodzi ndi iwe m’manja mwa Afilisiti,+ moti mawa iweyo+ ndi ana ako+ mukhala ndi ine. Komanso Yehova aperekadi asilikali a Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+ 1 Mbiri 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Sauli ndi ana ake atatu anafa,+ ndipo anthu onse a m’nyumba yake anafera limodzi.
19 Yehova aperekanso Isiraeli pamodzi ndi iwe m’manja mwa Afilisiti,+ moti mawa iweyo+ ndi ana ako+ mukhala ndi ine. Komanso Yehova aperekadi asilikali a Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+