1 Samueli 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afilisiti anayandikira kwambiri Sauli ndi ana ake, ndipo pamapeto pake anapha Yonatani,+ Abinadabu+ ndi Malikisuwa,+ ana aamuna a Sauli. 2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+
2 Afilisiti anayandikira kwambiri Sauli ndi ana ake, ndipo pamapeto pake anapha Yonatani,+ Abinadabu+ ndi Malikisuwa,+ ana aamuna a Sauli.
8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+