Genesis 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+ Yoswa 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Gawo lawo linayambira ku Mahanaimu+ kuphatikizapo dera lonse la Basana,+ ndi dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi mfumu ya Basana, ndiponso midzi yonse ing’onoing’ono ya Yairi+ ku Basana. Gawo lawoli linali ndi matauni 60 onse pamodzi. 2 Samueli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.
2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+
30 Gawo lawo linayambira ku Mahanaimu+ kuphatikizapo dera lonse la Basana,+ ndi dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi mfumu ya Basana, ndiponso midzi yonse ing’onoing’ono ya Yairi+ ku Basana. Gawo lawoli linali ndi matauni 60 onse pamodzi.
24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.