2 Samueli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye. Nyimbo ya Solomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwerera kuti tikuone!”+ “Kodi anthu inu mukuona chiyani mwa ine Msulami?”+ “Tikuona ngati tikuonerera gule wa magulu awiri a anthu.”
24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.
13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwerera kuti tikuone!”+ “Kodi anthu inu mukuona chiyani mwa ine Msulami?”+ “Tikuona ngati tikuonerera gule wa magulu awiri a anthu.”