Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+

  • Yoswa 13:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kuchokera ku Hesiboni+ linakafika ku Ramati-mizipe ndi ku Betonimu, ndiponso kuchokera ku Mahanaimu+ mpaka kumalire ndi Debiri.+

  • 2 Samueli 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena