2 Samueli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Sauli anali ndi mdzakazi, dzina lake Rizipa,+ mwana wamkazi wa Aya.+ Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “N’chifukwa chiyani unagona ndi mdzakazi*+ wa bambo anga?” 2 Samueli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Rekabu ndi Bana, ana aamuna a Rimoni Mbeeroti, ananyamuka kupita kunyumba ya Isi-boseti+ masana kutatentha, ndipo anamupeza akugona. 2 Samueli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake ndipo anapha Rekabu ndi Bana+ ndipo anadula manja ndi mapazi awo. Kenako anawapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni, koma anatenga mutu wa Isi-boseti ndi kuuika m’manda a Abineri ku Heburoni.+
7 Tsopano Sauli anali ndi mdzakazi, dzina lake Rizipa,+ mwana wamkazi wa Aya.+ Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “N’chifukwa chiyani unagona ndi mdzakazi*+ wa bambo anga?”
5 Rekabu ndi Bana, ana aamuna a Rimoni Mbeeroti, ananyamuka kupita kunyumba ya Isi-boseti+ masana kutatentha, ndipo anamupeza akugona.
12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake ndipo anapha Rekabu ndi Bana+ ndipo anadula manja ndi mapazi awo. Kenako anawapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni, koma anatenga mutu wa Isi-boseti ndi kuuika m’manda a Abineri ku Heburoni.+