Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 16:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi adzakazi a bambo ako+ amene wawasiya kuti azisamalira nyumba.+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa+ pamaso pa bambo ako,+ ndipo manja+ a anthu onse amene ali ndi iwe adzalimba ndithu.”

  • 2 Samueli 16:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho anamangira Abisalomu hema padenga,+ ndipo Abisalomu anayamba kugona ndi adzakazi a bambo ake,+ Aisiraeli onse akuona.+

  • 1 Mafumu 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mfumu Solomo itamva zimenezi inafunsa mayi ake kuti: “N’chifukwa chiyani mukum’pemphera Adoniyayu Abisagi Msunemu? M’pemphereninso ufumu+ (chifukwa iye ndi mkulu wanga).+ Mupemphereni ufumu Adoniyayo. Mupempherenso wansembe Abiyatara+ ndi Yowabu+ mwana wa Zeruya.”+

  • Miyambo 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amene amalangiza wonyoza amadzichotsera yekha ulemu,+ ndipo amene amadzudzula woipa amadzibweretsera chilema.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena