2 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.