2 Samueli 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adoramu+ anali kutsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 1 Mafumu 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Elihorefi ndi Ahiya, ana a Sisa, omwe anali alembi,+ ndi wolemba zochitika dzina lake Yehosafati,+ mwana wa Ahiludi. 1 Mbiri 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yowabu mwana wa Zeruya anali mkulu wa gulu lankhondo,+ ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
24 Adoramu+ anali kutsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
3 Elihorefi ndi Ahiya, ana a Sisa, omwe anali alembi,+ ndi wolemba zochitika dzina lake Yehosafati,+ mwana wa Ahiludi.
15 Yowabu mwana wa Zeruya anali mkulu wa gulu lankhondo,+ ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.