6 Kenako anthuwo anangoona mwamuna wina wachiisiraeli+ akubwera ndi mkazi wachimidiyani.+ Anali kubwera naye kufupi ndi abale ake, pamaso pa Mose ndi pamaso pa khamu lonse la ana a Isiraeli. Pa nthawiyi n’kuti Aisiraeliwo akulira pakhomo la chihema chokumanako.