Numeri 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Dzina la mwamuna wachiisiraeli, amene anaphedwa limodzi ndi mkazi wachimidiyani uja, linali Zimiri mwana wa Salu. Saluyo anali mtsogoleri+ wa nyumba ya makolo a Asimiyoni.
14 Dzina la mwamuna wachiisiraeli, amene anaphedwa limodzi ndi mkazi wachimidiyani uja, linali Zimiri mwana wa Salu. Saluyo anali mtsogoleri+ wa nyumba ya makolo a Asimiyoni.