Salimo 73:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho kudzikuza kuli ngati mkanda m’khosi mwawo,+Ndipo avala chiwawa ngati malaya.+ Miyambo 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pali m’badwo umene maso ake ali pamwamba kwambiri, ndiponso umene maso ake owala ali odzikweza.+ 1 Timoteyo 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+
24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+