Yesaya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,Ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo mofanana ndi anthu a ku Sodomu.+Iwo sanayese nʼkomwe kulibisa. Tsoka kwa iwo, chifukwa akudzibweretsera mavuto. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Yesaya 1, tsa. 57
9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,Ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo mofanana ndi anthu a ku Sodomu.+Iwo sanayese nʼkomwe kulibisa. Tsoka kwa iwo, chifukwa akudzibweretsera mavuto.