Maliro 3:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Inu Yehova, mudzawabwezera mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+ Hoseya 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa chakuti zimene iwe Isiraeli unachita zinali zotsutsana ndi ine mthandizi wako,+ zimenezo zidzakuwononga.+
9 Chifukwa chakuti zimene iwe Isiraeli unachita zinali zotsutsana ndi ine mthandizi wako,+ zimenezo zidzakuwononga.+