2 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo.
18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo.