1 Samueli 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Mhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ m’bale wake wa Yowabu, kuti: “Ndani atsike nane kupita kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nawe.”+ 2 Samueli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti awatsogolere pofola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+ 2 Samueli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anauza Abisai+ kuti: “Tsopano Sheba+ mwana wamwamuna wa Bikiri atisautsa kwambiri kuposa Abisalomu.+ Iweyo utenge atumiki+ a mbuye wako ndi kumuthamangitsa kuti asapeze mizinda ya mipanda yolimba kwambiri ndi kutizemba ife tikuona.” 1 Mbiri 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abisai+ m’bale wake wa Yowabu+ anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye ananyamula mkondo n’kupha anthu 300 ulendo umodzi, ndipo anali wotchuka ngati amuna atatu aja. 1 Mbiri 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti afole mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+
6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Mhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ m’bale wake wa Yowabu, kuti: “Ndani atsike nane kupita kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nawe.”+
10 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti awatsogolere pofola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+
6 Ndiyeno Davide anauza Abisai+ kuti: “Tsopano Sheba+ mwana wamwamuna wa Bikiri atisautsa kwambiri kuposa Abisalomu.+ Iweyo utenge atumiki+ a mbuye wako ndi kumuthamangitsa kuti asapeze mizinda ya mipanda yolimba kwambiri ndi kutizemba ife tikuona.”
20 Abisai+ m’bale wake wa Yowabu+ anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye ananyamula mkondo n’kupha anthu 300 ulendo umodzi, ndipo anali wotchuka ngati amuna atatu aja.
11 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti afole mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+