1 Mbiri 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ena onse anawapereka kwa mchimwene wake Abisai+ kuti awatsogolere pokamenyana ndi Aamoni.