1 Mbiri 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti afole mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+
11 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti afole mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+