1 Mbiri 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abisai+ m’bale wake wa Yowabu+ anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye ananyamula mkondo n’kupha anthu 300 ulendo umodzi, ndipo anali wotchuka ngati amuna atatu aja.
20 Abisai+ m’bale wake wa Yowabu+ anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye ananyamula mkondo n’kupha anthu 300 ulendo umodzi, ndipo anali wotchuka ngati amuna atatu aja.