Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Mhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ m’bale wake wa Yowabu, kuti: “Ndani atsike nane kupita kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nawe.”+

  • 2 Samueli 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti awatsogolere pofola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+

  • 2 Samueli 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma Abisai,+ m’bale wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu 30 amenewo. Iye ananyamula mkondo ndi kupha nawo anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+

  • 1 Mbiri 11:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Abisai+ m’bale wake wa Yowabu+ anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye ananyamula mkondo n’kupha anthu 300 ulendo umodzi, ndipo anali wotchuka ngati amuna atatu aja.

  • 1 Mbiri 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Nayenso Abisai+ mwana wa Zeruya,+ anapha Aedomu 18,000 m’chigwa cha Mchere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena