1 Samueli 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Mhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ m’bale wake wa Yowabu, kuti: “Ndani atsike nane kupita kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nawe.”+ 2 Samueli 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anakantha Mfilisitiyo ndi kumupha. Pamenepo asilikali a Davide analumbira kwa iye kuti: “Simudzapitanso ndi ife kunkhondo,+ chifukwa mungazimitse+ nyale+ ya Isiraeli!”
6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Mhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ m’bale wake wa Yowabu, kuti: “Ndani atsike nane kupita kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nawe.”+
17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anakantha Mfilisitiyo ndi kumupha. Pamenepo asilikali a Davide analumbira kwa iye kuti: “Simudzapitanso ndi ife kunkhondo,+ chifukwa mungazimitse+ nyale+ ya Isiraeli!”