2 Samueli 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamapeto pake Abisai mwana wa Zeruya+ anauza mfumu kuti: “N’chifukwa chiyani galu wakufa uyu+ akukunyozani mbuyanga mfumu?+ Ndiloleni ndipite chonde ndikam’dule mutu.”+ 2 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musachitire nkhanza+ mnyamatayo Abisalomu chifukwa cha ubwino wanga.” Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleri onsewa za nkhani yokhudza Abisalomu.
9 Pamapeto pake Abisai mwana wa Zeruya+ anauza mfumu kuti: “N’chifukwa chiyani galu wakufa uyu+ akukunyozani mbuyanga mfumu?+ Ndiloleni ndipite chonde ndikam’dule mutu.”+
5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musachitire nkhanza+ mnyamatayo Abisalomu chifukwa cha ubwino wanga.” Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleri onsewa za nkhani yokhudza Abisalomu.