12 Koma munthuyo anauza Yowabu kuti: “Ngakhale ndikanalandira ndalama 1,000 zasiliva m’manja mwanga, sindikanatambasula dzanja langa ndi kupha mwana wa mfumu. Pakuti ife tinamva mfumu ikukulamulani inuyo, Abisai ndi Itai kuti, ‘Aliyense wa inu ateteze mnyamatayo Abisalomu.’+