2 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musachitire nkhanza+ mnyamatayo Abisalomu chifukwa cha ubwino wanga.” Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleri onsewa za nkhani yokhudza Abisalomu.
5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musachitire nkhanza+ mnyamatayo Abisalomu chifukwa cha ubwino wanga.” Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleri onsewa za nkhani yokhudza Abisalomu.