-
2 Samueli 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Abineri atamva mawu amenewa a Isi-boseti anakwiya kwambiri+ n’kunena kuti: “Kodi ine ndine galu+ wopanda pake wa Yuda? Ineyo ndikusonyeza kukoma mtima kosatha ku nyumba ya Sauli bambo ako, abale ake ndi mabwenzi ake apamtima, ndipo ndikukuteteza kuti usagwe m’manja mwa Davide, koma lero ukundiimba mlandu wa cholakwa chokhudza mkazi.
-