1 Samueli 17:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+ 1 Samueli 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi mfumu ya Isiraeli ikulondola ndani? Kodi mukuthamangitsa ndani? Zoona mukuthamangitsa galu wakufa?+ Nthata imodzi?+ 2 Samueli 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamapeto pake Abisai mwana wa Zeruya+ anauza mfumu kuti: “N’chifukwa chiyani galu wakufa uyu+ akukunyozani mbuyanga mfumu?+ Ndiloleni ndipite chonde ndikam’dule mutu.”+
43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+
14 Kodi mfumu ya Isiraeli ikulondola ndani? Kodi mukuthamangitsa ndani? Zoona mukuthamangitsa galu wakufa?+ Nthata imodzi?+
9 Pamapeto pake Abisai mwana wa Zeruya+ anauza mfumu kuti: “N’chifukwa chiyani galu wakufa uyu+ akukunyozani mbuyanga mfumu?+ Ndiloleni ndipite chonde ndikam’dule mutu.”+