Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi mfumu ya Isiraeli ikulondola ndani? Kodi mukuthamangitsa ndani? Zoona mukuthamangitsa galu wakufa?+ Nthata imodzi?+

  • 2 Samueli 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?”

  • 2 Samueli 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamapeto pake Abisai mwana wa Zeruya+ anauza mfumu kuti: “N’chifukwa chiyani galu wakufa uyu+ akukunyozani mbuyanga mfumu?+ Ndiloleni ndipite chonde ndikam’dule mutu.”+

  • 2 Mafumu 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Hazaeli atamva mawu amenewa, anati: “Ndine ndani ine mtumiki wanu, galu ngati ine,+ kuti ndichite zinthu zazikulu ngati zimenezi?” Koma Elisa anati: “Yehova wandionetsa iweyo utakhala mfumu ya Siriya.”+

  • Luka 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti aliyense wodzikweza adzatsitsidwa, ndipo wodzichepetsa adzakwezedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena