1 Samueli 17:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+ 2 Samueli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?” Salimo 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Landitsani moyo wanga ku lupanga,+Moyo wanga wokhawu umene ndili nawo muulanditse m’kamwa mwa galu.+
43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+
8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?”
20 Landitsani moyo wanga ku lupanga,+Moyo wanga wokhawu umene ndili nawo muulanditse m’kamwa mwa galu.+