1 Samueli 17:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+ 2 Samueli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?” Miyambo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zotsatirapo za kudzichepetsa ndiponso kuopa Yehova ndizo chuma, ulemerero, ndi moyo.+ Mateyu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense wodzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense wodzichepetsa adzakwezedwa.+
43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+
8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?”