1 Samueli 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wako m’manja mwako.+ Ndiye ndilole chonde, ndimubaye ndi kumukhomerera pansi ndi mkondo kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.” Luka 9:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ophunzira ake, Yakobo ndi Yohane,+ ataona zimenezi anati: “Ambuye, kodi mukufuna tiwaitanire moto+ kuchokera kumwamba kuti uwanyeketse?” Aroma 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+
8 Tsopano Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wako m’manja mwako.+ Ndiye ndilole chonde, ndimubaye ndi kumukhomerera pansi ndi mkondo kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.”
54 Ophunzira ake, Yakobo ndi Yohane,+ ataona zimenezi anati: “Ambuye, kodi mukufuna tiwaitanire moto+ kuchokera kumwamba kuti uwanyeketse?”
19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+