1 Mafumu 18:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Atatero, moto+ wa Yehova unatsika n’kunyeketsa nsembe yopsereza+ ija, nkhuni, miyala ndi fumbi lomwe. Unaumitsanso madzi amene anali m’ngalande muja.+ 2 Mafumu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Eliya anayankha mtsogoleri wa asilikali 50 uja kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu, moto+ utsike kumwamba n’kunyeketsa iweyo ndi asilikali ako 50.” Ndipo moto unatsikadi kumwamba n’kunyeketsa mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.+
38 Atatero, moto+ wa Yehova unatsika n’kunyeketsa nsembe yopsereza+ ija, nkhuni, miyala ndi fumbi lomwe. Unaumitsanso madzi amene anali m’ngalande muja.+
10 Koma Eliya anayankha mtsogoleri wa asilikali 50 uja kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu, moto+ utsike kumwamba n’kunyeketsa iweyo ndi asilikali ako 50.” Ndipo moto unatsikadi kumwamba n’kunyeketsa mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.+